KODI MLANDU WANU ULI BWANJI (Booklet)

You might also like

Download as pdf or txt
Download as pdf or txt
You are on page 1of 6

Ndipo anati kwa ine, Mau awa ali

okhulupirika ndi oona; ndipo Ambuye Mulungu


wa mizimu ya aneneri, anatuma mngelo wache
kukaonetsera akapolo ache zimene ziyenera
kuchitika msanga. Ndipo Taonani ndidza
msanga. Wodala iye amene asunga mau a
chinenero cha Buku ili. Iye wakukhala
wosalungama achitebe zosalungama; ndi
munthu wonyansa akhalebe wonyansa; ndi iye
amene ali woyera akhalebe woyeretsedwa.”— “Nthawi zakusadziwako tsono Mulungu analekelera; koma
Chibvumbulutso 22:6,7,11.
tsopanotu ali mkulamulira anthu ponse ponse atembenuke
mtima; chifukwa anapangiratu tsiku limene adzaweruza
dziko lokhalamo anthu m’chilungamo, ndi Munthu amene
anamuikiratu; napatsa anthu onse chitsimikizo, pamene
anamuukitsa kwa akufa.” Machitidwe 17:30, 31.

12 1
Mau Oyamba: yonse, werengani Yesaya 40:25, 26; 45:18; Masalmo 100:3; 95:6; Chibvu. 4:11.
Ndipo ulosi waonetsera gulu lina lomwe chifukwa cha Uthenga uwu, akusunga
Malamulo a Mulungu. Limodzi la Malamulo awa limaloza mwachindunji kwa
KODI MLANDU WANU ULI BWANJI TSOPANO? Mulungu monga Mlengi,
“...Koma Tsiku lachisanu ndichiwiri ndilo Sabata la Yehova
“Kodi mlandu wanu uli bwanji tsopano?” Ndilo funso lomwe Mulungu Wako. Pakuti Masiku asanu ndi limodzi Yehova ana-
limafunsidwa kwa munthu amene ali ndi mlandu ku bwalo loweruza maliza zakumwamba ndi zapansi, ndi nyanja, ndi zinthu
zonse ziri m’menemo; napumula Tsiku Lachisani ndi chiwiri;
womwe ukudikiridwa chigamulo molingana ndi zomwe zipezeke mu chifukwa chache Yehova anadalitsa Tsiku la Sabata kuti
kafukufuku wa mlanduwu. likhale lopatulika.” Exsodo 20:10, 11. Zokhuzana ndi
Muphunziro ili tikhala tikulingalira pa mutu umenewu.
Koma mwina mkumafunsa kuti, kodi ndiye kuti tonse tili ndi milandu Chotero Sabata
kubwalo loweruza? ndilo chikumbutso cha chilengedwe lomwe limaonet-
Mu muku Lopatulika timapeza zitsanzo zingapo zomwe mkwiyo wa sera chifukwa choona chokhacho chomwe ulemu wonse uyenera kupita kwa
Mulungu unafika pa anthu a kusamvera atatha kuchenjezedwa kuti Mulungu Yekha. Mwaichi lamulo la Sabata ndi pomwe pagonera maziko enieni a
alape ndipo kumapeto kwa kuumitsa mitima yawo ndinso kumapeto kupembedza koona kwa umulungu. Kusunga kwa Sabata ndiko chizindikiro cha
kwa nthawi yachisomo ya chipiliro cha Mulungu pa iwo Mulungu kumvera kwathu kwa Mulungu Woona. Kusalisunga ndi kulowesapo m’malo
mwake sabata lina losalamulidwa ndi Malemba Opatulika ndiko chizindikiro cha
anagwetsa ziweruzo. Mulungu asanaononge dziko loyamba Nowa
mpanduko wotsiritsa wonenedwa mu ulosi.
mlaliki wa chilungamo analalika kwa zaka 120 kuchenjeza za
chiweruziro chilimkudza ndi kuika poyera njira yothawirapo. Koma Ambuye Mulungu wa mtentendere atidalitse kuti tikadziwe chomwe tiyenera
ambiri sanamvere kufikira chigumula chinadza nichinawaononga iwo. kuchita pamene tikukhala nthawi ya chiweruziro yomwe posakhalitsa iyenera
Sodom ndi Gomola asanaonongeke machenjezo anapita kwa anthu kutsekedwa chotero Iye akunena, “Ngati ndikondwera nayo imfa ya woipa? Ati
opandukirawo kuti aturuke koma ambiri ananyalanyaza kufikira moto Ambuye, Si ndiko abwelere kuleka njira yache yoipa ndi kukhala ndi moyo?
unawanyeketsa onse. Pochoka ku Aigputo Mulungu anawapatsa ana a Chifukwa chache ndidzakuweruzani inu …..yense monga mwa njira zache, Ati
Israyeli malonjezano, Malamulo, Malemba ndi Maweruzo komanso Ambuye yehova. Bwelereani nimutembenuke kuleka zolakwa zanu zonse, ndipo
anawachitira zozizwa zambiri. “Pakuti sindifuna abale kuti mukhale simudzakhumudwa nazo ndi kuonongeka nayo Mphulupulu.Tayani ndi kuzi-
chotsera zonyansa zanu zonse munalakwa nazo ndi kuzifunira mtima watsopano,
osadziwa, kuti makolo athu onse anali pansi pa mtambo, naoloka
ndi mzimu watsopano….” Ezekiel 18:23, 30-32. Amen
nyanja onse, nabatizidwa onse kwa Mose, mu mtambo ndi m’nyanja,
nadya onse chakudya chauzimu chimodzimodzi; namwa onse
Ngati Mukufuna Maphunziro Oonjezera pa Phunziro Ili kapena Maphunziro ena
chakumwa chauzimu chimodzimodzi; pakuti anamwa mwa Thanthwe
Lumikizanani Nafe Kudzera Ku
lauzimu la kuwatsata; koma Thanthwero ndiye Khristu. Koma ochuruka
a iwo Mulungu sanakondwera nawo; pakuti anamwazika m’chipululu.
General Conference Ya Mpingo Wa Malawi Union
Koma zinthu izi zinachitika, zikhale zotichenjeza ife kuti International Missionary Society International Missionary Society
tisalakelake zoipa, monga iwonso analakalaka. Kapena musakha- S.D.A Reform Movement Seventh-Day Adventist Church
le opembedza mafano, monga ena a iwo, monga kwalembedwa, An- 265 West Avenue Reform Movement
thu anakhala pansi kudya ndi kumwa nanyamuka nasewera. Kapena Cedartown, GA 3021—USA Off Chinsapo Road
tisachite dama monga ena a iwo anachita dama, nagwa tsiku Telephone (+1) 770-7480077 P.O. Box 100
limodzi zikwi makumi awiri ndi zitatu. Kapena tisayese Ambuye Fax (+1) 770-7480095 Likuni—Lilongwe Malawi
monga ena a iwo anayesa, naonongeka ndi njoka zija. Kapena musa- Email—info@sda 1844. org Email:malawiunion@hotmail.com
dandaula, monga ena a iwo anadandaula, naonongeka ndi woonon- Internet: www. Sda 1844. org.
gayo. Koma izi zinachitika kwa iwowa monga zotichenjeza, ndipo
Kapena imbani lamya pa nambala zotsatirazi:
zinalembedwa kutichenjeza ife, amene matsirizidwe a nthawi ya
pansi pano adzafike pa ife. Chifukwa chache iye wakuyesa kuti
+265 995 133 455- +265 888 018 950—Kumpoto
ali chiliri, ayang’anire kuti angagwe.” 1 Akorinto 10:1-11.
+265 999 681 358- +265 999 084 577 —Pakati
0996 166 043 – +265 999 666 018—Kumwela
—Osindikiza
MW Union Publishing Association-0994 551 560

2 11
Kotero ichi pokhala cholinga (Goal) chomwe kumwamba konse kukufu-
na kuchifikira, Mulungu mwachifundo chake watumiza Uthenga KODI MLANDU WANU ULI BWANJI TSOPANO?
wosatha kudziko lonse kwa anthu amitundu ndi manenedwe onse,
monga taona kale mau a Ambuye kuti Uthenga uwu womwe uli ndi
choonadi chakupulumutsa udzalalikidwa padziko lonse kuti ukhale Mu Phunziroli tikhala tikukambirana kudzera m’mafunso
umboni kuti pamene chiwerizo chotsiridza chikudza anthu adzasowe ndi mayankho kuchokera M’buku lopatulika
chowiringula.
VESI LOTSOGOLERA: Deotronomo 32: 28, 29.—Popeza iwo
KUOPA MULUNGU NDI KUMPATSA ULEMELERO: Pofuna kuopa Mulun- ndiwo mtundu wa anthu wosowa uphungu konse, ndipo
gu ndi kumpatsa ulemelero anthu akuyenera kumvera Lamulo lake. Wanzeruyo alibe chidziwitso. 39 Akadakhala nazo nzeru
akuti, “Opani Mulungu, musunge Malamulo ake: pakuti choyenera anthu onse
ndi ichi.” Mlaliki 12:13. Opanda kumvera ku Malamulo ake, palibe kupembedza
akadazindikira ichi, akadasamalira chitsiridziro chawo.
komwe kungakhale kokondweretsa Mulungu. “Muli abwenzi anga ngati muchita
zimene ndikuuzani.” “Ngati mukonda Ine, sungani Malamulo anga.” “Pakuti ichi 1. Kodi mau oti “Chiweruzo” amatanthauzanji? Buku lotan-
ndi chikondi cha Mulungu, kuti tisunge Malamulo ache.” “Wopewetsa khutu
lache kuti asamve chilamulo, ngakhale pemphero lache linyansa.” Yohane
thauzira zilankhulo (Dictionary) la Oxford limatanthauza
15:14; 14:15; 1 Yohane 5:3; Miyambo 28:9. Zotsatira za kumvera Uthenga uwu mauwa monga “kuthekera kopanga ganizo lolingaliridwa
zaperekedwa m’mau, “Pano pali chipiliro cha Oyera mtima, Awa ndiwo kapena kupanga ganizo lanzeru,” “ganizo kapena kuphera
akusunga Malamulo a Mulungu ndi chikhulupiliro cha Yesu.” Chibv. 14:12. mkota,” “ganizo la bwalo la lamulo kapena woweruza.”
Pofuna kuti anthu akakonzekere chiweruziro iwo akuyenera kusunga Malamulo
a Mulungu, “….Pakuti onse amene anachimwa podziwa lamulo; adzaweruzidwa
ndi lamulo, Tsiku limene Mulungu adzaweruza ndi Yesu Khristu zinsisi za an- Polingalira za matanthauzo awa tiyeni tilingalireninso chimene
thu.” Aroma 2:12, 16. chimachitika wina akakhala ndi mlandu ku bwalo loweruza.
Kodi chofunikira ndichiyani pofuna kusunga Lamulo la Mulungu? Koma po-
funa kusunga Lamulo la Mulungu pafunika chikhulupiliro, Pakuti “opanda  Mlandu ulionse kuti uchitike umakhala ndi anthu awa:
chikhulupiliro sikutheka kumkondweretsa Mulungu.” Ndipo chilichonse chom- Wolakwa, Woweruza, Mboni, ngakhalenso Loya.
we sichili muchikhulupiliro ndi uchimo.” Ahebri 11:6; Aroma 14:23.
 Polingalira zonse zomwe zimachitika kudziko lapansi
KUYAMBA KWA ORA LACHIWERUZIRO: Kuyamba kwa ora pamene wina ali ndi mlandu tiyeni tsono chidwi chathu
lachiweruziro uku kukuloza nthawi imene Khristu Wansembe wathu Wamkuru chipite m’Buku Lopatulika, kodi Baibulo likutinji za
analowa m’chipinda chopatulikitsa cha Kachisi wakumwamba ndi kukayamba chitsiliziro cha anthu onse?
ntchito ya utumiki m’malo mwa munthu ndi chiweruzo chofufuza kufikira
nthawi imene ntchitoyi idzathe. Ntchitoyi ikuyenera kupitilira kufikira milandu
ya onse akufa ndi amoyo omwe itaganiziridwa kuti yayenera imfa kapena moyo. 2. Kodi ndizoona kuti tonse tikuyenera kukumana ndi
Kotero idzatseka ndi kutsekedwa kwa nthawi yachifundo pamene Khristu chiweruzo?
Wansembe Yemwe waima patsogolo pa Likasa Lachipangano m’mwamba 2 Akorinto 5:10.—Pakuti ife tonse tiyenera kuonetsedwa ku Mpan-
adzaime ndi kulengeza “Kwatha, Iye wakukhala wosalungama achitebe do wa kuweruza wa Khristu, kuti yense alandire zochitika m’thupi,
zosalungama ndi munthu wonyansa akhalebe wonyansa, ndi iye wakukhala monga momwe anachita, kapena zabwino kapena zoipa.
wolungama achitebe cholungama, ndi iye amene ali woyera akhalebe woyeret-
sedwa.” Chibvu. 22:11. Panthawi iyi milandu ya onse idzakhala itaganiziridwa,
chisomo chomwe chaperekedwa kwa anthu kwa nthawi yaitali kuti akonze 3. Kodi cholinga cha Mulungu potumiza Mwana wache
ntchito zawo chidzakhala chitatsekedwa, sikudzakhalanso kulapa komwe kud- kudziko lapansi chinali chiyani?
zalandire chikhululukiro, lero lino nthawi yachifundo yaperekedwa kwa onse Yohane 3:16, 17; 12:47.—Pakuti Mulungu anakonda dziko lapansi,
kukakonzekera nthawi yoopsayi monga inaperekedwera ku m’bado wa Nowa kotero kuti anapatsa Mwana wache wobadwa Yekha, kuti yense
chigumula chisanafike. wakukhulupilira Iye asataike koma akhale nawo moyo wosatha.
17Pakuti Mulungu sanatuma Mwana wache kudziko lapansi kuti
KUPEMBEDZA MLENGI: Udindo Wopembedza Mulungu waikidwa pansi pa
akaweuze dziko lapansi, koma kuti dziko lapansi likapulumutsidwe
mfundo yonena kuti Iye ali Mlengi ndipo zinthu zonse zichokera kwa Iye.
Paliponse m’Baibulo Mulungu akufunsa kumpembedza pamwamba pa milungu ndi Iye. 12:47Ndipo ngati wina akumva Mau anga, ndi kuwasunga, Ine

10 3
sindimuweruza; pakuti sindinadza kudzaweruza dziko lapansi, koma 11. Podziwa kuti Malamulo a Mulungu ndiwo myeso pomwe
kuti ndikapulumutse dziko lapansi. Werenganinso Machitidwe 10:42, 43. makhalidwe a anthu akuyesedwa muchiweruzo kumwamba,
kodi ndi chenjezo lotsiridza liti lomwe likupita kwa mtundu
4. Ngati Mulungu anatuma Mwana wache kudzapulumutsa dziko ulionse, manenedwe, ndi anthu padziko lonse?
osati kuweruza, nanga ndichifukwa chiyani pali chiweruzo? Chibvumbulutso 14:6, 7.—Ndipo ndinaona mngelo wina akuuluka
Yohane 3:19, 20.—Koma chiweruzo ndi ichi, kuti kuunika kunadza ku pakati pa mlengalenga, wakukhala nawo Uthenga Wabwino
dziko lapansi, ndipo anthu anakonda mdima koposa kuunika; pakuti Wosatha, aulalikire kwa iwo akukhala padziko, ndi kwa mtundu
ntchito zawo zinali zoipa. 20Pakuti yense wakuchita zoipa adana nako ulionse, ndi kwa pfuko ndi manenedwe ndi anthu; ndi kunena ndi
kuunika, ndipo sadza ku kuunika, kuti zingatsutsidwe ntchito zache. mau aakuru, Opani Mulungu, mpatseni ulemnelero; pakuti yafika
nthawi ya chiweruziro chache; ndipo mlambireni Iye amene
analenga m’mwamba ndi mtunda ndi nyanja ndi akasupe amadzi.
MITUNDU YA CHIWERUZIRO
Chiweruzo cha mlandu chimachitika m’magawo atatu: —Mu uthenga uwu muli mbali zisanu zomwe tizifotokoze bwino
lomwe mwa tsatane-tsatane:
1. Uthenga Wosatha
1) Kufufuza Kwa Mlandu [Chiweruzo chofufuza] 2. Wopita kwa anthu padziko lonse
Iyi ndi ndondomeko ya chiweruzo yomwe imaphatikizirapo 3. Kuopa Mulungu ndi kumpatsa ulemelero
kufufuza kwa maumboni a mlandu ndi kuzenga mlandu. 4. Kuyamba kwa ora la Chiweruziro
1) Kupanga Chitsimikizo [Ganizo] 5. Kupembedza Mlengi
Mlandu utatha kufufuzidwa ndi kuzengedwa, woweruza
amapanga chitsimikizo kapena ganizo molingana ndi UTHENGA WOSATHA: Uthenga uwu ukubwera munthawi yoyenera
kauniuni wa maumboni onse, apa ndi pomwe munthu ndipo waonetsedwa kuti ukuyenera kulalikidwa munthawi yakumapeto
amatsimikiziridwa mbali yomwe ali kaya wolakwa kapena pofuna kuwakonzetsera anthu kudzanso kwachiwiri kwa Ambuye.
wosalakwa molingana ndi amumboni opezedwa. Ambuye pofotokoza za zizindikiro za kudza kwake anati kuti chimariziro
3) Chilango [chigamulo] cha dziko chisanafike, “Uthenga uwu Wabwino wa Ufumu udzalalikidwa
Mlandu utatha kufufuzidwa kenako ndikutsimikizilidwa kuti pa dziko lonse lapansi ukhale umboni kwa anthu a mitundu yonse ndipo
pomwepo chidzafika chimariziro.” Mateyu 24:14.
wokhuzidwayo ndiwolakwadi kenako woweruza amapereka
Uthengawu ukutchedwa uthenga wosatha chifukwa uli ndi
chigamulo kapena chilango kwa wolakwayo. choonadi chosatha cha nthawi ino chomwe sichinalalikidwepo, komanso
ukutchedwa wosatha chifukwa choonadi chomwe Uthengawu ulinacho
5. Monga wansembe wamkuru wa Kachisi wongoimilira wa Chipan- chili chamuyaya ndi chosasinthika. Poloza ku choonadi ichi Ambuye
gano Chakale amalowa muchipinda chopatulikitsa kamodzi pa- ananena: “Musaganize kuti ndinadza kudzapasula chilamulo kapena
chaka (Levitiko 16:1, 29, 30; Ahebri 9:7), kukatetezera aneneri, sindinadza kupasula koma kukwaniritsa. Pakuti indetu
mphulupulu za ana a Israyeli, Kodi lero lino Wansembe Wathu ndinena kwa inu, kufikira litapita thambo ndi dziko, kalemba
Wamkuru Yesu Khristu ali kuti ndipo akugwira ntchito yanji: kakang’ono kamodzi, kapena kansonga kake kamodzi sikadzachoka ku
Ahebri 8:1, 2.—Koma mutu wa izi tanenazi ndi uwu: Tiri naye Mku- chilamulo…..Mateyu 5:17, 18. Ndipo Atakwera kumwamba akutsindikanso
ruwansembe Wotere, amene anakhala pa Dzanja lamanja la Mpando kudzera mwa Yohane mneneri, “Ndichita umboni kwa munthu aliyense wa-
wachifumu wa Ukulu m’Kumwamba, Mtumiki wa Malo opatulikitsa, ndi kumva mau a chinenero cha Buku ili, Munthu akaonjeza awa, adzamuonjezera
wa chihema choona, chimene Ambuye anachimanga si munthu ayi. Mulungu miliri yolembedwa m’buku ili, ndipo aliyense akachotsako…. Mulungu
Yohane 5:22.—Pakuti Atate saweruza munthu aliyense, koma ana- adzamuchotsera gawo lache pa Mtengo wa Moyo….. Chibv. 22:18, 19.
pereka kuweruza konse kwa Mwana.
WOPITA KWA ANTHU PADZIKO LONSE: Cholinga cha Mulungu kwa
6. Kodi limodzi mwa machenjezo otsiliza a Mulungu kudziko likuti anthu onse chafotokozedwa pa 1 Timoteyo 2:3, 4 “Pakuti ichi nchokoma
tikukhala masiku anji, ndipo molingana ndi nthawiyi tikuyenera ndi cholandirika pamaso pa Mulungu Mpulumutsi wathu; amene afuna
kuchita chiyani? anthu onse apulumuke, nafike pozindikira choonadi.

4 9
manyado, zisangalatso, ndi zongozionetsera, zonsezi zimalembedwa Chibvumbulutso 14:6, 7. Ndipo ndinaona mngelo wina ali kuuluka pa-
mosaphophonya m’mabuku a mbiri akumwamba. kati pa mlengalenga, wakukhala nawo Uthenga Wabwino wosatha,
—Tchimo lirilonse lochitidwa mwanseri, wochitayo atha kuchita zoipazo aulalikire kwa iwo akukhala padziko, ndi kwa mtundu ulionse ndi
m’kuwala kwausana kaya mu mdima wausiku, koma zimakhala pfuko lililonse ndi manenedwe ndi anthu; ndi kunena ndi mau
zotseguka pamaso pa Iye amene amaona paliponse. Angelo a Mulungu aakuru, Opani Mulungu, mpatseni ulemelero; pakuti yafika nthawi
amachitira umboni ndi kulembera uchimo ulionse mu zolembera ya chiweruziro chake; ndipo Mlambireni Iye amene analenga
zosaphophonya. m’mwamba ndi mtunda ndi nyanja ndi akasupe amadzi.
—Tchimo litha kubisidwa, kukanidwa, ndi kuphimbidwa kuti
lisadziwike kwa abambo, amayi, kwa mkazi, kwa mwamuna, kwa ana, 7. Kodi Nthawi yachiweruziro yomwe tikukhalayi inayamba nthawi
kwa abwenzi kapena ku mpingo, koma limaikidwa mooneka pamaso pa yanji?
mzeru zakafukufuku zakumwambazo. Mdima waukuru wausiku, zinsisi Danieli 8:14.—Nati kwa Ine mpaka masiku zikwi ziwiri mphambu
zobisidwa mwaluso ndi achinyengo sizili zokwanira kubisikika pamaso mazana atatu (2 300) usana ndi usiku; pamenepo Malo Opatulika
pa chidziwitso cha Mulungu Wamphambuyonseyo. Anthu atha adzayesedwa olungama.
kunyengedwa, ndi kupusitsidwa ndi iwo a mtima wachinyengo, koma ZOTI TIDZIWE: Nthawi yachiweruziroyi inayamba pamene Yesu
Mulungu amapyoza zobisika m’mtima ndi kuwerenga moyo wam’kati, analowa mu Malo Opatulikitsa a Kachisi Wakumwambakuyamba
Iye sanyengedwa ndi maonekedwe a munthu, chuma, maphunziro, kugwira ntchito monga Wansembe Wamkuru. (Kutambasulidwa kwa
kapena kulankhula kochenjeretsa kapena koonetsera chiyero kwa nthawiyi kwafotokozedwa bwino mu zowerenga zathu zina).
anthu. Mbiri ya zochita za munthu aliyense kaya zabwino kapena zoipa
imatoledwa mosamalitsa bwino ngati kuti kumwamba konse kunali
chidwi pa munthu m’modzi kuyang’anitsitsa zochita zache. Tsopano KUKUMANA NDI MBIRI YA MOYO
kodi mlandu wako m’bale kapena mlongo ulibwanji?
8. Kodi ndi Tsiku liti loopsa lomwe
MUYESO WA CHIWERUZIRO linaonetsedwa kwa Danieli
Mneneri pamene makhalidwe ndi
10. Kodi ndi myeso uti womwe Woweruza miyoyo ya anthu onse zinadutsa
Wadziko lonse akugwiritsa ntchito moonedwanso Pamaso pa
kuyeza makhalidwe a munthu aliyse? Woweruza wa dziko lonse?
Mlaliki 12:13, 14.—Mau atha zonse
zamveka zatha, opani Mulungu, musunge Danieli 7:9, 10, 13, 14.—Ndinapenya
Malamulo ache; pakuti choyenera anthu mpaka anaikapo mipando Yachifumu,
onse ndi ichi. Pakuti Mulungu adzanena nikhalapo Nkhalamba Yakale lomwe,
mlandu wa zochita zonse, ngakhale zabwino, ngakhale zoipa. zovala zache zinali za mbuu ngati
Yakobo 2:10, 12.—Pakuti amene chipale chofewa, ndi tsitsi lapamutu pache ngati ubweya woyera, Mpando
aliyense angasunge Malamulo onse, Wachifumu unali Malawi a moto, ndi njinga zache moto woyaka. 10Msinje
wamoto unayenda woturuka pamaso pache, zikwi zikwi anamtumikira, ndi
koma akakhumudwa pa limodzi, unyinji wosawerengeka unaima pamaso pake, Woweruza mlandu anakhala-
iyeyu wachimwira onse. … Motero po, ndi mabuku anatsegulidwa. 13Ndinaona m’masomphenya a usiku, tanani
lankhulani, ndipo chitani motero anadza ndi mitambo yakumwamba wina ngati Mwana wa munthu, nafika
monga anthu amene adzaweruzidwa kwa Nkhalamba ya kale lomwe; ndipo anamyandikizitsa pamaso pache. 14N-
ndi Lamulo laufulu. dipo anampatsa ulamuliro, ndi ulemelero, ndi Ufumu, kuti anthu onse, ndi
ZOTI TIDZIWE: Malamulo a Mulungu mitundu yonse ya anthu ndi a manenedwe onse, amtumikire; ulamuliro
ndiwo myeso pamene makhalidwe ndi wache ndi ulamuliro wosatha wosapitilira, ndi ufumu wache sudzaonongeka.
miyoyo ya anthu onse zikuyezedwa
muchiweruziro chofufuza, pakuti Mal- ZOTI TIDZIWE: Zinaonetsedwa kwa mnener i Tsiku lalikur u ndi loophsa pamene
amulo a Mulungu ndiwo amene miyoyo ndi makhalidwe a anthu onse zidzadutse pamaso pa Mulungu. Nkhalamba ya
amavumbulutsa khalidwe lake. kale lomwe ndiye Mulungu Atate Yemwe ali chiyambi cha zolengedwa zonse (Masalmo 90:2),

8 5
Iye ndiye ali wopereka Malamulo chotero ndiye amene akutenga mbali —Nchitidwe ulionse wozipereka nsembe chifukwa cha Khristu, ntchito zonse zachifundo
mu chiweruzo. Ndipo Angelo Oyera zikwi khumi kupinda zikwi khumi zochitidwa kwa osauka, ozunzika, amasiye zochitidwa ndi mtima wopanda undekha ndi
akutumikira pamaso pake monga mboni pa bwalo lalikuru la cholinga chopatulika zimalembedwa mokhulupirika.
chiweruziroli. Kudza kwa Mwana wa munthu amene ali Yesu komwe
kwafotokozedwa pa vesi 13 ndi 14 si kudza kwake kwachiwiri kudziko —Zunzo, vuto, yeso, chitonzo, chiphsinjo, ndi chisoni zilizonse zopiliridwa chifukwa
lapansi. Iye akudza kwa Nkhalamba Ya kale lomwe (Mulungu Atate), cha Dzina la Khristu, zonse zimalembedwa mokhulupirika. Atero Davide, “Muwerenga
motsogozedwa ndi angelo akumwamba Wansembe wathu wamkuru kuthawathawa kwanga, Sungani misonzi yanga msupa yanu; kodi siikhala
akulowa m’chipinda Chopatulikitsa cha Kachisi wakumwamba kuka- m’Buku mwanu?” Masalmo 56:8. Zonsezi zimalembedwa mokhulupirika
onekera pamaso pa Mulungu ndipo Mulungu anamuyandikizitsa chifupi mu Buku Lachikumbukiro ndi Dzanja lomwe diso lake limaona ponse-
ndi Iye kuti ampatse ulamuliro ndi mphamvu kukachita chochitika cho- ponse ndipo ngakhale munthu atataidwa ndipo kulira ndi kubuula
maliza cha utumiki wake m’malo mwa munthu—kukachita ntchito ya kwake palibe khutu likumumva, ndipo palibe dzanja liri lokonzeka
chiweruzo chofufuza ndi kupembedzera onse amene akhale opindulako kumuthandiza koma pali m’modzi Yekhayo yemwe amaona ngakhale
ku mwazi wake wokhetsedwa pamtanda chifukwa cha machimo awo. kuvutika ndi kulira kwa mpheta zakuthengo, ameneyo amaona ndipo
amalemba mokhulupirika bwino zunzo lonse lopiliridwa kuyembekezera
9. Kodi ndi mabuku ati momwe mumalembedwa maina ndi mbiri kuti lidzalandire mphotho yake yachilungamo. Kaya pali ena akuchita
ya zochita zonse za munthu aliyese kaya zobisika kapena ntchito yabwino yachilungamo, ingakhale yochepetsetsa ndi yonyozeka
zoonekera omwe adzatsimikizire ganizo la chiweruzo? m’maso mwa munthu motani kotero kuti palibe kamwa yoturutsa mau
a chiyamikiro kuntchitoyo, koma alipo Wina amene amawerenga
ZOTI TIDZIWE: Danieli 7:10 akuti, “Chiweruziro chinaikidwa ndipo Mabuku kukhulupirika konse ameneyo amalemba nsembe yochitidwa ndi mtima
anatsegulidwq,” Buku Lopatulika linanena za mabuku atatu momwe wopanda undekha iliyonse ndipo idzalandira mphotho yachilungamo.
kumwamba kumalemba Mbiri ya zochita za munthu aliyense kuchokera
nthawi yake yobadwa kufikira imfa yake, mabukuwa ndi awa: 3. BUKU LAMACHIMO: Mlaliki 12:14; Mateyu 12:36, 37.—Pakuti
Mulungu adzanena mlandu wa zochita zonse, ndi zobisika zonse,
1. BUKU LA MOYO: Chibvumbulutso 20:12.— Buku lina ngakhale zabwino, ngakhale zoipa. Ndipo ndinena kwa inu, kuti mau
linatsegulidwa, ndilo Buku la moyo: ndipo akufa anaweruzidwa mwa onse opanda pache amene anthu adzalankhula, adzawerengeredwa
zinthu izo zolembedwa m’mabuku, molingana ndi ntchito zawo. mlandu wache Tsiku lakuweruza. Pakuti udzayesedwa wolungama
—Buku la moyo mumakhala maina a onse amene alandira choonadi ndi mau ako, ndipo ndi mau ako omwe udzatsutsidwa.
chopulumutsa ndi kulowa mu utumiki wake. Yesu ananena kwa
akuphunzira ake atangochoka ku utumiki, ‘Koma kondwerani kuti maina Palinso mbiri yolembedwa ya machitachita onse oipa ndi osalungama:
anu alembedwa m’mwamba.’ Paulo Mtumwinso akufotokoza za ogwira —Zolinga ndi zifukwa zonse zachinsisi, zimalembedwa ndi Dzanja
ntchito anzake okhulupirika, “Amene maina awo ali M’buku la moyo.” Afili- losaphophonyalo, Mtumwi akuchitira umboni kuti, Chifukwa chache
pi 4:3. Yohane M’bvumbulutsi nayenso akuti iwo amene adzalowe mu musaweruze kanthu isanadze nthawi yache, kufikira akadze Ambuye
Mzinda wa Mulungu ndiwo amene “maina awo alembedwa M’buku la moyo amenenso adzaonetsera zobisika za mdima, nadzasonyeza zitsimikizo za
la Mwanawankhosa.” Chibvumbulutso 21:27. Werenganinso Danieli 12:1.
mtima…” 1 Akorinto 4:5. Ndipo Ambuye alankhula kwa onse ochita
zoipa naona ngati akubisala, “Taonani, chilembedwa pamaso panga;
2. BUKU LACHIKUMBUKIRO: Malaki 3:16.—Pamenepo iwo akuopa Y ehova
analankhulana wina ndi mnzache; ndipo Yehova anawatchera khutu namva, ndipo
sindidzakhala chete, koma ndidzabwezera, … Zoipa zanu pamodzi ndi
Buku Lachikumbutso linalembedwa Pamaso Pache la iwo akuopa Yehova, nakumbukira zoipa za makolo anu, Atero Yehova.” Yesaya 65:6, 7.
Dzina lache. —Moyang’anizana ndi dzina la munthu aliyense m’mabuku
—Buku Lachikumbukiro mumalembedwa ntchito zabwino za iwo akuopa Mulungu, akumwamba kumalembedwa ndi zitsimikizo zoopsa za liwu lirilonse
nakumbukira pa Dzina lache. loipa, nchitidwe uliwonse waundekha, ntchito iliyonse yosakwanilitsid-
—Mau awo achikhulupiliro, achikondi, achifundo, amalembedwa m’mwamba. Nehemiya wa, machenjezo ndi zidzudzulo zotumizidwa ndi kumwamba zomwe
anali kutanthauza ku ichi pamene anati, “Mundikumbukire zanyalanyazidwa, kusalabadiridwa ndi kukanidwa, mphindi zongotaid-
Mulungu Wanga, mwaichi musafafanize zokoma zanga ndinazichitira Nyumba ya
wa ndi zinthu zachabe, m’mwayi yosapambanitsidwa kuubwino, zikoka
Mulungu wanga…” Nehemiya 13:14.
—Mu Buku Lachikumbukiro chochita chilichonse chachilungamo chimalembedwa. Yeso zoipa, zonsezi zimalembedwa mosutsana ndi wochitayo.
lirilonse lokanizidwa, choipa chilichonse cholakidwa, liu lolimbikitsa ena zonse —Ndalama, nthawi, ndi mphamvu zoperekedwa nsembe pofuna kukwa-
zimalembedwa mokhulupirika. niritsa zikhumbokhumbo zaumunthu, zoonongedwera ku ma fashoni,
6 7

You might also like