DGBV

You might also like

Download as docx, pdf, or txt
Download as docx, pdf, or txt
You are on page 1of 7

Nkhanza kwa Amayi

Written by

Ismail. A Juneja

1
FADE IN:

INT. BEDROOM - DAYLIGHT

MERCY feels unwell. She calls ANDREW, her husband on his


cellphone. He is away from home.

Phone rings.

CONTINUOUS’
EXT. ROADSIDE - DAYLIGHT

Andrew awaits for SADRA (his side chick). The carries a


jumbo loaded with some staff. He stares at his ringing
phone; looks around and puts back the phone in his
pocket. He has no interest on her wife’s call. It rings
again until Sandra arrives. He immediately rejects the
call and turns the phone off.

SANDRA
Nawesotu Andrew umandipatsa befu.
Moti upange zaine uli busy ndi
mkazi wako opanda mbuyo uja.

ANDREW
Aaa, iwe alibe ntchito amene uja
pano ndikupanga za iweyo mpaka
madzulo ano.

CONTINUOUS’
INT. BEDROOM - DAYLIGHT

Mercy calms no more.

MERCY
Koma bambo akufuna ndiganize bwanji.
Kapenatu ali mu meeting ija amati
ichitika masana ano. Koma anakango
tumiza text yachangu ija yoti
“in a meeting” basi. Kusiyana ndi
achitazi. Komatu ine sindikumva
bwino. Hmmm, mwina ndipumeko.

Mercy lays herself down.

EXT. ROADSIDE - DAYLIGHT

The two (Andrew and Sandra) bid goodbye to each other.

2
ANDREW
Tsono ukatere usowe kwa three days.
Yako ija ine kusowa ngakhale text
yako. Kaya ndimalakwa chani kaya.

SANDRA

Hehehehe.. iwe umakahala busy ndi


Mercy nde ndidzikuvutitsa. Mesa
banja patsogolo kaye.

ANDREW
Sandra umadziwa chani.Ulendo uno
sindikumphweketsa ngakhale pang’ono.

SANDRA
Tionera pa inu. Ndipo chaka chatha
mpaka anzanga onse akwatiwa. Hmmm
Chino chikangothaso, ndukuza
ndikwatiwa ndi amene angamaone
kufunika kwanga.

Sandra gets angry with Andrew.

ANDREW
Ukudziwa Sandra, a Lumbe akundigulitsa
malo akulu bwino. Pa rent patopetsa
mami.

MERCY(Anger torment her)


Ukakhale ndi kadzidzi wakoyotu?

Sandra gets very angry.

ANDREW
Sandra! Sandra! Ndimakukondatu ine.
Chilipo chomwe sindinakupangirepo?
Unakafunsa bwino za malo ndikugulawo
cholinga chomwe ndikugulira osati
kundipitira kutsogolo komwe kusali
m’maganizo.

SANDRA
Andrew usandikweze BP pansewu pano.
Ndakupatsa miyezi itatu. Ukapanda
kukathamangitsa ka nanzikambe kako
kaja uiwale za ine. Ndipo malowo
alembedwe m’dzina la mwana
ameneyu (points her belly).

3
Sandra leaves the site. At the same moment Andrew faces
down.

ANDREW
(Mono dialogue)

(Sighs)Ndipange bwanji chifukwa


Sandra ndimankonda nde sindingalore
ndidzimuona ena atamutenga.

Andrew things for a moment and walks away in deep


thoughts.

INT. ANDREW’S RESIDENCE - EVENING

Andrew opens the door, gets in and sits down on a chair.


Mercy still sleeps at the bedroom. After a few minutes,
Andrew gets out of the chair, walks to the kitchen, finds
out that Mercy is not there. He opens the lids of some
pots only to find out that food has been cooked. He walks
to the bedroom.

ANDREW
Hey! What rubbish is this?
Ukutani?
SANDRA
Dad ndalakwaso chani?

ANDREW
Usandifunse. Sukuona cholakwa?
Mkazi wapa banja amayenera
kumatakataka every time.

SANDRA
Dad sindikupeza bwino nthupi.
Ndakuimbirani masana koma munaidula.
Ndimafuna ndikudziwitseni mene
ndikumvera nthupi. Oti mpaka pano
sizikusintha.

ANDREW
Iwetu ukumazolowera kunama masiku
ano.

Andrew achotsa chofunda.

ANDREW
Ukamafuna kulenga bodza kapena nthenda,
ukuzinamiza. Akazi anzeru komaso ufuna

4
banja amapanga zofuna za amuna awo osati
bodza lakolo. Tadzuka apa usanaone
nyenyezi.

Mercy wakes up helplessly.

ANDREW
Upite ukandigawire chakudya. Nyamuka!
Akazi opusa amapasula banja lawo ndi
manja awo. Umadziwa? He!

MERCY
Eya ndimadziwa koma dad sindikupeza...

ANDREW

Fwefwefwe... ndine, ndikuswatu.


Kapena sizinamveke ndanenazi?

MERCY
Ayi zamveka dad. Pepani ndithu.

Mercy walks to the kitchen and as she arrives Andrew


shouts...

ANDREW
Mercy!

MERCY
(loud-trying voice)
Dad.

Mercy arrives at the bedroom.

MERCY
Ine dad, ndamva kuitana.

ANDREW (Removes his shoes)


Undisiyire nsapato zangazi apo.

Mercy does what she has been told.

ANDREW
Kunakolopedwa kuno?

MERCY
Eya dad. Kawiri konse munandiuzira.

Andrew slips his finger along the floor.

ANDREW(Shows Mercy his finger)

5
Ukuona fumbili. Nde wakolopa pati?
Kukolopedwe kuno ndisanagone.

MERCY
Chabwino dad.

ANDREW
Uchotseso akangaude lero lomwe.
Makamaka uyambirire akangaudewo
usanakolope. Zamveka?

MERCY
Eya dad ndamva. Komatu kunabwera
A Lumbe madzulo omwe ano. Amakamba
za...

ANDREW
(Panting heavily)
Zisakukhudze! Foolish woman.
Upange chomwe unauzidwa pakhomo
pano. Nkhani zinazi zisamakukhaudze.
Apo bii, udzanyamuka.

MERCY
Pepani dad. Mundukhululukire.

ANDREW (Stretching his arm)


Ukasiye pa charge phone yangayi.

MERCY
Chabwino dad.

ANDREW
Usayelekeze kugwiragwira foniyo
ndinagula ndi ndalama zanga. Nanga
inu ndi kupanda sukuluku mumaidziwa
redmi. Mukamva choncho mumaona
ngati ndi mgonero mu chichewa.
Chimene umadziawa iwe ndi bread,
kudya basi. Makolo ako anakulekerera
ukadali wang’ono.

MERCY
(Breathing sadly)
Dad, ndikhoza kupita kukakonza
chakudya?

ANDREW
(Staring heavily)
Tadzipitani apa. Watsala ndi masiku
owerengeka m’nyumba muno udziwe zimenezi.

6
Mercy hardly walks after she hears these words. She
leaves Andrew’s site.

ANDREW
(Loud voice)
Komaso uyerekeze kugona pa mpandopo.
Ukagona panja.

Andrew looks around the bedroom.

CONTINUOUS’
Mercy face looks gloomy as she goes to serve her husbands
food.

MERCY (V.0)
Kodi banja lija ndi limeneli?
Ndikulakwa pati Ambuye?
Nkhaza zolapitsa pa moyo wanga.
Ndalira mumtima. Anzanga ambiri
amandisilira, anakadziwa za mumtima.

THE END

You might also like