Download as pdf or txt
Download as pdf or txt
You are on page 1of 3

NYIMBO YOTSIRIZA 239

Tili ndi Mtendere


Wopambanatu
Monga ngati mtsinje
Mumitimamo,
Koma mtsinje uno
Umayenda phee,
Nthawi zonse mtima
Nutonthozabe.

Tikakhulupira
Mlungu wathuyo
Tidzaona mwayi
Ndi mtenderewo

Dzanja la Mulungu
Litisunga nji!
Nkhondo ya Satana
Sitiopa ‘yi’
Zaphokoso zonse
Ndi zoopsyazo
Sizibvuta mtima
Sizilowamo.

Masauko athu
Ndi zokondwazo
Azilola zonse
Ndi Atatewo
Pokhulupirira
Tidzapezabe
Kuti mtima wake
Utikonda ‘fe’
NDONDOMEKO YA MAPEMPHERO MPINGO
WOTSOGOLERA: Rev. Henry B. Mtema 13.Chopereka
14.Mwambo opereka mphatso
1. Nyimbo yoyamba: 191
 Mr. Limbani Karanya
2. Mau achikhazikitso
3. Pemphero: Rev. Henry B. Mtema  Presbytery
4. Salimo lovomerezana: Salimo 23: 1-6  Azibusa ndi Amayi Busa onse
5. Makwaya  Chilumba CCAP: Mpingo, Milaga,
6. Zolengeza: Makomiti,
 Alembi a Mpingo Makwaya ndi
 Alembi a Presbytery Akhristu onse
7. Kuwerenga mau a Mulungu  Onse oitanidwa ndi akufuna kwabwino
15.Kudalitsa
 Chipangano chakale: Genesis 13: 1-13
zopereka:……………………………………………
 Chipangano cha tsopano: Yohane 14: 27-31
….
8. Chikhulupiriro cha Atumwi: Mpingo onse
16.Zolankhula:
9. Pemphero
lachiwiri:…………………………………………..  Alembi a Mpingo
10.Nyimbo ya mzimu oyera: 105  Amfumu
11.Ulaliki: Rev. Jimmy Banda  MP: Hon. Orphan Shaba
12.Mwambo omasula Abusa.  Abusa otsanzika: Rev. Jimmy Banda
 Oyimira Presbytery
 Oyimira Synod
17.Nyimbo yotsiriza: 239
18.Mdalitso:…………………………………………….
.
19.Mawu omaliza: Mr. Juma Kalaje
(wapampando wa Organising
committee)

END OF PROGRAM
NYIMBO YOYAMBA 191 NYIMBO YA CHIWIRI 105

Idzani, Mzimu inu


Ambiri tikondwera mwa Yesu
Mundidalitse kuno
Nanga inu? Nanga inu?
Ndafooka mtima ine
Tapeza Chipulumutso ndithu
Polendo wanga uno
Nanga inu? Nanga inu?
Kwambiri ndakhumudwa
Panjirayo ya moyo
Masiku onse timakondwera
Mkaleka kutsogola
Pakumva mawu ake a Yesu
Ndiwonongeka pompo.
Wolalikira tidzamumvera
Nanga inu? Nanga inu?
Wakunga mwana ine
Sindidziwitsa konse
Ife tiyembekezera Yesu
Mundilandize Mzimu
Nanga inu? Nanga?
Panjira yanga yonse
Chimwemwecho chili mu mtimamu
Mundiyendetse bwino
Nanga inu? Nanga inu?
Ndifike ine ndemwe
Panjira yolungama
Titasokera tinabwerera
Ku dziko la chimwemwe.
Nanga inu? Nanga inu?
Tadziwa kuti ndiwo uchimo
Mundilimbitse m’mtima
Nanga inu? Nanga inu?
Pogwira ntchito izi
Ndikapumula pena
Tinachoka munjira ya imfa
Mukhale ndithu ndine
Nanga inu? Nanga inu?
Zolingilira zanga
Takopeka ndi mawu a Yesu
Ziyere zonse m’mtima
Nanga inu? Nanga inu?
Zoipa muzichotse
Sindidzazichitanso.

You might also like